Album Photo

Recent Activities

Chiphatikizo cha nyimbo zimene zinayimbidwa ku Area 36 SDA Church pa 15th October 2022 tsiku limene kunkatsekeredwa Revival.
Chipulumutso ndi udindo wa munthu aliyense payekha payekha. Tonse choti tichite tikuchidziwa ndipo tikuyenera kuchita zimenezi pakusayang'ana kuti wina akutani. Kugwa ndi kulephera kwa anthu ena...
Mumpingo wa Yehovah muli magulu anayi omwe ali; adani, atinke nawo, ana a Mulungu ndi akhristu olema.
Chifupikitso cha mauthenga onse amu Pulumuka ndi moyo wako Digital Crusade komanso kuyankha mafunso amene anthu amafunsa.