Day 5: Muli imfa nkhalimo (Revival)

Ngakhale mu mpingo umene uli wa Yehovah, zimafika nyengo ndi nthawi mmene zinthu zimalakwika ndipo ndi udindo wathu ife tonse monga ziwalo za mpingo kukonza zinthu koma mosamalitsa ndi kusalozana zala.
Posted by ITC Ministries in Series on November 06 2022 at 11:28 PM  ·  Public
Comments (0)
No login
Login or register to post your comment