Day 5: Tisamalitse pa nkhani zodetsedwa (Pulumuka ndi moyo wako Digital Crusade)

Mulungu akufuna anthu ake tidzisiyanitsa pakati pa zinthu zodetsedwa ndi zinthu zabwino-bwino ndipo tidzichita mosamara ndi zinthu zimene zili zodetsedwa.
Posted by ITC Ministries in Series on November 14 2022 at 10:09 PM  ·  Public
Comments (0)
No login
Login or register to post your comment