Day 11: Thawani nkwiyo wa Yehovah (Pulumuka ndi moyo wako Digital Crusade)

Pamene dziko likupita ku mapeto, dziko lapansi lipanga umodzi koma owukila Mulungu wa kumwamba ndipo kuyikidwa malamulo atsopano kudziko lapansi omwe akhale otsutsana ndi Mulungu. Ndipo Mulungu alanga wina aliyense amene atalowe nawo muzochitika zimenezi ndi mirili isanu ndi iwiri.
Posted by ITC Ministries in Series on November 15 2022 at 12:00 AM  ·  Public
Comments (0)
No login
Login or register to post your comment