Day 1: Mbiri ya mpingo (Revival)

Dziko lapansi litachimwa lilekana ndi Mulungu, Mulungu anapanga njila yoti anthu tibwererenso kwa Iye, tiyanjanenso naye ndipo tiyambenso kuyenda naye ndi kukhala naye. Ndipo Mulungu anafuna kukwanilitsa chimenechi kudzera mukagulu ka anthu kotchedwa mpingo.
Posted by ITC Ministries in Series on November 06 2022 at 10:34 PM  ·  Public
Comments (0)
No login
Login or register to post your comment