Chipulumutso ndi udindo wa munthu aliyense payekha payekha. Tonse choti tichite tikuchidziwa ndipo tikuyenera kuchita zimenezi pakusayang'ana kuti wina akutani. Kugwa ndi kulephera kwa anthu ena...