Day 7: Pulumuka ndi moyo wako (Revival)

Chipulumutso ndi udindo wa munthu aliyense payekha payekha. Tonse choti tichite tikuchidziwa ndipo tikuyenera kuchita zimenezi pakusayang'ana kuti wina akutani. Kugwa ndi kulephera kwa anthu ena kusatilepheletse kukafika ku Yerusalemu watsopano.
Posted by ITC Ministries in Series on November 16 2022 at 12:27 AM  ·  Public
Comments (0)
No login
Login or register to post your comment