Mulungu sadzayang'anila uchimo umene anthu tikuchita mpaka muyaya. Tsiku likudza lomwe alilange dziko lapansi. Kodi akamalilanga dziko lapansi, inu mukhala muli mbali iti?