19. Day 19 Kaphiri SDA Church Crusade Thawani mkwiyo wa Yehovah

Mulungu sadzayang'anila uchimo umene anthu tikuchita mpaka muyaya. Tsiku likudza lomwe alilange dziko lapansi. Kodi akamalilanga dziko lapansi, inu mukhala muli mbali iti?
Posted by Rhessah Mponda in Series on February 03 2024 at 06:53 PM  ·  Public
Comments (0)
No login
Login or register to post your comment